Aroma 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mundiperekere moni kwa Purisika ndi Akula,+ antchito anzanga potumikira Khristu Yesu. 1 Akorinto 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni. Akula ndi Purisika komanso mpingo umene umasonkhana mʼnyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa nonsenu, mwa Ambuye.
19 Mipingo ya ku Asia ikupereka moni. Akula ndi Purisika komanso mpingo umene umasonkhana mʼnyumba mwawo,+ akupereka moni wochokera pansi pa mtima kwa nonsenu, mwa Ambuye.