Aefeso 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mulungu watsegula mitima yanu nʼcholinga choti muone komanso mudziwe chiyembekezo chimene wakupatsani ndiponso zinthu zabwino kwambiri zimene walonjeza kwa oyera,+ Akolose 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 komanso muzithokoza Atate, amene anapangitsa kuti mukhale oyenerera kulandira nawo cholowa cha oyera+ amene ali mʼkuwala.
18 Mulungu watsegula mitima yanu nʼcholinga choti muone komanso mudziwe chiyembekezo chimene wakupatsani ndiponso zinthu zabwino kwambiri zimene walonjeza kwa oyera,+
12 komanso muzithokoza Atate, amene anapangitsa kuti mukhale oyenerera kulandira nawo cholowa cha oyera+ amene ali mʼkuwala.