Machitidwe 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Paulo anayangʼanitsitsa Khoti Lalikulu la Ayudalo nʼkunena kuti: “Anthu inu, abale anga, ndachita zinthu popanda chikumbumtima changa kunditsutsa ngakhale pangʼono pamaso pa Mulungu+ mpaka lero.” 1 Akorinto 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mumtima mwanga sindikudzitsutsa pa nkhani iliyonse. Koma zimenezi sizikutanthauza kuti basi ndine wolungama, chifukwa Yehova* ndi amene amandifufuza.+ Aheberi 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pitirizani kutipempherera, chifukwa tikukhulupirira kuti tili ndi chikumbumtima choyera* ndipo tikufuna kuchita zinthu zonse moona mtima.+
23 Paulo anayangʼanitsitsa Khoti Lalikulu la Ayudalo nʼkunena kuti: “Anthu inu, abale anga, ndachita zinthu popanda chikumbumtima changa kunditsutsa ngakhale pangʼono pamaso pa Mulungu+ mpaka lero.”
4 Mumtima mwanga sindikudzitsutsa pa nkhani iliyonse. Koma zimenezi sizikutanthauza kuti basi ndine wolungama, chifukwa Yehova* ndi amene amandifufuza.+
18 Pitirizani kutipempherera, chifukwa tikukhulupirira kuti tili ndi chikumbumtima choyera* ndipo tikufuna kuchita zinthu zonse moona mtima.+