Machitidwe 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Patatha masiku 5, kunafika mkulu wa ansembe Hananiya+ pamodzi ndi akulu ena, komanso munthu wina wodziwa kulankhula,* dzina lake Teritulo. Iwo anayamba kufotokoza mlandu wa Paulo kwa bwanamkubwa.+
24 Patatha masiku 5, kunafika mkulu wa ansembe Hananiya+ pamodzi ndi akulu ena, komanso munthu wina wodziwa kulankhula,* dzina lake Teritulo. Iwo anayamba kufotokoza mlandu wa Paulo kwa bwanamkubwa.+