Machitidwe 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma anandiuzabe kuti, ‘Nyamuka, chifukwa ndidzakutumiza kutali kwa anthu a mitundu ina.’”+ Aroma 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano ndikulankhula ndi inu anthu a mitundu ina. Popeza ndine mtumwi wotumidwa kwa anthu a mitundu ina,+ ndimalemekeza utumiki wanga,+
13 Tsopano ndikulankhula ndi inu anthu a mitundu ina. Popeza ndine mtumwi wotumidwa kwa anthu a mitundu ina,+ ndimalemekeza utumiki wanga,+