1 Akorinto 15:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndi mmenenso zilili ndi kuuka. Thupi limene limakwiriridwa limakhala loti lingawonongeke, koma limene limaukitsidwa limakhala loti silingawonongeke.+ 1 Akorinto 15:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Monga zilili kuti panopa tikufanana ndi wopangidwa ndi dothi uja,+ tidzafanananso ndi wakumwambayo.+
42 Ndi mmenenso zilili ndi kuuka. Thupi limene limakwiriridwa limakhala loti lingawonongeke, koma limene limaukitsidwa limakhala loti silingawonongeke.+
49 Monga zilili kuti panopa tikufanana ndi wopangidwa ndi dothi uja,+ tidzafanananso ndi wakumwambayo.+