Yeremiya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kodi pali mtundu uliwonse wa anthu umene unasinthapo milungu yawo nʼkuyamba kulambira milungu imene kulibeko? Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zopanda phindu.+ Machitidwe 17:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Choncho, popeza ndife ana a Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa ndi anthu aluso.+
11 Kodi pali mtundu uliwonse wa anthu umene unasinthapo milungu yawo nʼkuyamba kulambira milungu imene kulibeko? Koma anthu anga asinthanitsa ulemerero wanga ndi zinthu zopanda phindu.+
29 Choncho, popeza ndife ana a Mulungu,+ tisaganize kuti Mulunguyo ali ngati golide, siliva, mwala kapena chilichonse chosemedwa ndi anthu aluso.+