Aroma 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Khalani akhama osati aulesi.+ Yakani ndi mzimu.+ Tumikirani Yehova* monga akapolo.+