Yohane 8:31, 32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiyeno Yesu anapitiriza kuuza Ayuda amene anamukhulupirirawo kuti: “Mukapitiriza kusunga mawu anga, ndiye kuti ndinudi ophunzira anga. 32 Mudzadziwa choonadi+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+ Yakobo 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma amene amayangʼanitsitsa mulamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu ndipo amapitiriza kuliyangʼanitsitsa, adzakhala wosangalala ndi zimene akuchita+ chifukwa chakuti si munthu amene amangomva nʼkuiwala, koma amene amachita zimene wamvazo.
31 Ndiyeno Yesu anapitiriza kuuza Ayuda amene anamukhulupirirawo kuti: “Mukapitiriza kusunga mawu anga, ndiye kuti ndinudi ophunzira anga. 32 Mudzadziwa choonadi+ ndipo choonadi chidzakumasulani.”+
25 Koma amene amayangʼanitsitsa mulamulo langwiro+ limene limabweretsa ufulu ndipo amapitiriza kuliyangʼanitsitsa, adzakhala wosangalala ndi zimene akuchita+ chifukwa chakuti si munthu amene amangomva nʼkuiwala, koma amene amachita zimene wamvazo.