Yohane 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mukhale ogwirizana ndi ine ndipo inenso ndikhala wogwirizana ndi inu. Mofanana ndi nthambi imene singabereke zipatso payokha, pokhapokha ngati ili yolumikizikabe kumpesawo, inunso simungabereke zipatso pokhapokha ngati muli olumikizika kwa ine.+
4 Mukhale ogwirizana ndi ine ndipo inenso ndikhala wogwirizana ndi inu. Mofanana ndi nthambi imene singabereke zipatso payokha, pokhapokha ngati ili yolumikizikabe kumpesawo, inunso simungabereke zipatso pokhapokha ngati muli olumikizika kwa ine.+