Machitidwe 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Inu ndinu ana a aneneri ndi a pangano limene Mulungu anapangana ndi makolo anu akale.+ Iye anauza Abulahamu kuti: ‘Kudzera mwa mbadwa* yako mabanja onse apadziko lapansi adzadalitsidwa.’+ Machitidwe 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anamupatsanso pangano la mdulidwe.+ Kenako anabereka Isaki+ ndipo anamudula pa tsiku la 8.+ Nayenso Isaki anabereka* Yakobo ndipo Yakobo anabereka mitu ya mabanja 12 ija.
25 Inu ndinu ana a aneneri ndi a pangano limene Mulungu anapangana ndi makolo anu akale.+ Iye anauza Abulahamu kuti: ‘Kudzera mwa mbadwa* yako mabanja onse apadziko lapansi adzadalitsidwa.’+
8 Anamupatsanso pangano la mdulidwe.+ Kenako anabereka Isaki+ ndipo anamudula pa tsiku la 8.+ Nayenso Isaki anabereka* Yakobo ndipo Yakobo anabereka mitu ya mabanja 12 ija.