Yohane 8:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Iwo anamuyankha kuti: “Atate wathu ndi Abulahamu.” Yesu anawauza kuti: “Mukanakhala ana a Abulahamu,+ bwezi mukuchita ntchito za Abulahamu. Agalatiya 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiponso ngati muli ophunzira a Khristu, ndinudi mbadwa* za Abulahamu,+ olandira cholowa+ mogwirizana ndi lonjezolo.+
39 Iwo anamuyankha kuti: “Atate wathu ndi Abulahamu.” Yesu anawauza kuti: “Mukanakhala ana a Abulahamu,+ bwezi mukuchita ntchito za Abulahamu.
29 Ndiponso ngati muli ophunzira a Khristu, ndinudi mbadwa* za Abulahamu,+ olandira cholowa+ mogwirizana ndi lonjezolo.+