9 ndiponso kuti ndizionedwa kuti ndine wotsatira wake. Sikuti ndine wolungama chifukwa chakuti ndikuchita zonse moyenera potsatira Chilamulo, koma chifukwa chakuti ndimakhulupirira+ Khristu.+ Chilungamo chimenechi ndi chochokera kwa Mulungu ndipo chimabwera chifukwa cha chikhulupiriro.+