Yoweli 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka,+Chifukwa mʼphiri la Ziyoni ndiponso mu Yerusalemu mudzakhala anthu opulumuka+ ngati mmene Yehova ananenera.Anthu opulumuka amene Yehova akuwaitana.” Machitidwe 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo aliyense woitana pa dzina la Yehova* adzapulumuka.”’+
32 Ndipo aliyense woitana pa dzina la Yehova adzapulumuka,+Chifukwa mʼphiri la Ziyoni ndiponso mu Yerusalemu mudzakhala anthu opulumuka+ ngati mmene Yehova ananenera.Anthu opulumuka amene Yehova akuwaitana.”