37 Ngakhale kuti anachita zizindikiro zambiri pamaso pawo, iwo sankamukhulupirira, 38 moti mawu a mneneri Yesaya anakwaniritsidwa. Iye anati: “Yehova, kodi ndi ndani amene wakhulupirira zinthu zimene anamva kwa ife?+ Ndipo kodi dzanja la Yehova laonetsedwa kwa ndani?”+