2 Akorinto 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Okondedwa, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi ndi mzimu,+ kuti tikhale oyera pamene tikuopa Mulungu. 1 Petulo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mofanana ndi Woyera amene anakuitanani, inunso khalani oyera mʼmakhalidwe anu onse,+
7 Okondedwa, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi ndi mzimu,+ kuti tikhale oyera pamene tikuopa Mulungu.