Aroma 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mulungu anamupereka ngati nsembe yoti anthu agwirizanenso ndi Mulunguyo+ pokhulupirira magazi ake.+ Anachita zimenezi pofuna kuonetsa chilungamo chake chifukwa anasonyeza kuti ndi wosakwiya msanga pokhululuka machimo amene anachitika kale.
25 Mulungu anamupereka ngati nsembe yoti anthu agwirizanenso ndi Mulunguyo+ pokhulupirira magazi ake.+ Anachita zimenezi pofuna kuonetsa chilungamo chake chifukwa anasonyeza kuti ndi wosakwiya msanga pokhululuka machimo amene anachitika kale.