Afilipi 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Musamade nkhawa ndi chinthu chilichonse.+ Mʼmalomwake, nthawi zonse muzipemphera kwa Mulungu, muzimuchonderera kuti azikutsogolerani pa chilichonse ndipo nthawi zonse muzimuthokoza.+ 1 Atesalonika 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzipemphera nthawi zonse.+
6 Musamade nkhawa ndi chinthu chilichonse.+ Mʼmalomwake, nthawi zonse muzipemphera kwa Mulungu, muzimuchonderera kuti azikutsogolerani pa chilichonse ndipo nthawi zonse muzimuthokoza.+