Aroma 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene amadya chilichonse, asamanyoze amene sadya, ndipo wosadyayo asamaweruze amene amadya chilichonse,+ popeza iye analandiridwa ndi Mulungu. 1 Akorinto 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho kudziwa zinthu kwako kungachititse kuti uwononge munthu wofookayo, yemwe ndi mʼbale wako amene Khristu anamufera.+
3 Amene amadya chilichonse, asamanyoze amene sadya, ndipo wosadyayo asamaweruze amene amadya chilichonse,+ popeza iye analandiridwa ndi Mulungu.
11 Choncho kudziwa zinthu kwako kungachititse kuti uwononge munthu wofookayo, yemwe ndi mʼbale wako amene Khristu anamufera.+