Maliko 10:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Chifukwa ngakhale Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuti awombole anthu ambiri.”+ Yohane 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ine sindingachite chilichonse chimene ndangoganiza pandekha. Ndimaweruza mogwirizana ndi zimene ndamva, ndipo chiweruzo changa nʼcholungama,+ chifukwa sindichita zofuna zanga, koma zofuna za amene anandituma.+
45 Chifukwa ngakhale Mwana wa munthu sanabwere kudzatumikiridwa koma kudzatumikira+ ndi kudzapereka moyo wake dipo* kuti awombole anthu ambiri.”+
30 Ine sindingachite chilichonse chimene ndangoganiza pandekha. Ndimaweruza mogwirizana ndi zimene ndamva, ndipo chiweruzo changa nʼcholungama,+ chifukwa sindichita zofuna zanga, koma zofuna za amene anandituma.+