Salimo 119:49, 50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Kumbukirani mawu amene* munandiuza ine mtumiki wanu,Mawu amene mumandipatsa nawo chiyembekezo.* 50 Izi ndi zimene zimandilimbikitsa ndikakhala pamavuto,+Chifukwa mawu anu andithandiza kuti ndikhalebe ndi moyo. Aheberi 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma Khristu anali mwana ndipo ankayangʼanira nyumba ya Mulungu mokhulupirika.+ Ife tikhalabe nyumba ya Mulunguyo+ tikapitiriza kukhala ndi ufulu wa kulankhula komanso kugwira mwamphamvu chiyembekezo chimene timachinyadira mpaka mapeto. 1 Petulo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aneneri amene analosera za kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu anakusonyezani, anafufuza za chipulumutso chimenechi mwakhama ndiponso mosamala kwambiri.+
49 Kumbukirani mawu amene* munandiuza ine mtumiki wanu,Mawu amene mumandipatsa nawo chiyembekezo.* 50 Izi ndi zimene zimandilimbikitsa ndikakhala pamavuto,+Chifukwa mawu anu andithandiza kuti ndikhalebe ndi moyo.
6 Koma Khristu anali mwana ndipo ankayangʼanira nyumba ya Mulungu mokhulupirika.+ Ife tikhalabe nyumba ya Mulunguyo+ tikapitiriza kukhala ndi ufulu wa kulankhula komanso kugwira mwamphamvu chiyembekezo chimene timachinyadira mpaka mapeto.
10 Aneneri amene analosera za kukoma mtima kwakukulu kumene Mulungu anakusonyezani, anafufuza za chipulumutso chimenechi mwakhama ndiponso mosamala kwambiri.+