Miyambo 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndi ndani anganene kuti: “Ndayeretsa mtima wanga.+Ndine woyera ku tchimo langa”?+ Mlaliki 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa padziko lapansi palibe munthu wolungama amene amachita zabwino nthawi zonse ndipo sachimwa.+
20 Chifukwa padziko lapansi palibe munthu wolungama amene amachita zabwino nthawi zonse ndipo sachimwa.+