Machitidwe 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhulupirira Ambuye pamodzi ndi anthu onse a mʼbanja lake. Ndipo anthu ambiri a ku Korinto, amene anamva uthenga wabwino, anayamba kukhulupirira nʼkubatizidwa.
8 Kirisipo,+ mtsogoleri wa sunagoge, anakhulupirira Ambuye pamodzi ndi anthu onse a mʼbanja lake. Ndipo anthu ambiri a ku Korinto, amene anamva uthenga wabwino, anayamba kukhulupirira nʼkubatizidwa.