Aroma 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ine sindichita manyazi ndi uthenga wabwino.+ Kunena zoona, uthengawo ndi njira yamphamvu imene Mulungu akuigwiritsa ntchito pofuna kupulumutsa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba Ayuda+ kenako Agiriki.+
16 Ine sindichita manyazi ndi uthenga wabwino.+ Kunena zoona, uthengawo ndi njira yamphamvu imene Mulungu akuigwiritsa ntchito pofuna kupulumutsa aliyense amene ali ndi chikhulupiriro,+ choyamba Ayuda+ kenako Agiriki.+