-
2 Atesalonika 3:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndipotu inuyo mukudziwa zimene mukuyenera kuchita potitsanzira,+ chifukwa sitinachite zinthu zosalongosoka pakati panu, 8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.*+ Mʼmalomwake, tinagwira ntchito mwakhama komanso ndi mphamvu zathu zonse usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+
-