1 Akorinto 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma munthu wokonda zinthu zamʼdziko* savomereza* zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa, chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu. 1 Akorinto 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu asamadzinamize. Ngati aliyense wa inu akuganiza kuti ndi wanzeru nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru.
14 Koma munthu wokonda zinthu zamʼdziko* savomereza* zinthu za mzimu wa Mulungu, chifukwa amaziona ngati zopusa ndipo sangathe kuzidziwa, chifukwa zimafuna kuzifufuza mwauzimu.
18 Munthu asamadzinamize. Ngati aliyense wa inu akuganiza kuti ndi wanzeru nthawi* ino, akhale wopusa kuti akhale wanzeru.