Machitidwe 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Popeza ntchito yawo inali imodzi, anakhala kunyumba kwawoko. Iwo ankagwirira ntchito limodzi,+ chifukwa onse anali opanga matenti. Machitidwe 20:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Inunso mukudziwa bwino kuti manja awa anagwira ntchito kuti ndipeze zofunika pa moyo wanga+ ndi za amene ndinali nawo. 1 Akorinto 4:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mpaka pano tikadali anjala,+ aludzu+ ndiponso ausiwa. Tikumenyedwabe,+ tikusowabe pokhala 12 ndipo tikugwirabe ntchito mwakhama ndi manja athu.+ Akamatinenera zachipongwe, timadalitsa+ ndipo akamatizunza, timapirira moleza mtima.+ 2 Atesalonika 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.*+ Mʼmalomwake, tinagwira ntchito mwakhama komanso ndi mphamvu zathu zonse usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+
3 Popeza ntchito yawo inali imodzi, anakhala kunyumba kwawoko. Iwo ankagwirira ntchito limodzi,+ chifukwa onse anali opanga matenti.
34 Inunso mukudziwa bwino kuti manja awa anagwira ntchito kuti ndipeze zofunika pa moyo wanga+ ndi za amene ndinali nawo.
11 Mpaka pano tikadali anjala,+ aludzu+ ndiponso ausiwa. Tikumenyedwabe,+ tikusowabe pokhala 12 ndipo tikugwirabe ntchito mwakhama ndi manja athu.+ Akamatinenera zachipongwe, timadalitsa+ ndipo akamatizunza, timapirira moleza mtima.+
8 kapena kudya chakudya cha wina aliyense kwaulere.*+ Mʼmalomwake, tinagwira ntchito mwakhama komanso ndi mphamvu zathu zonse usiku ndi usana kuti aliyense wa inu asatilipirire kanthu kalikonse pofuna kutithandiza.+