Aroma 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa ngati mukukhala motsatira zofuna za thupi, ndiye kuti mosakayikira mudzafa.+ Koma mukalola kuti mphamvu ya mzimu ikuthandizeni kupha zochita za thupi, mudzakhala ndi moyo.+ Akolose 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho chititsani ziwalo za thupi lanu+ padziko lapansi kukhala zakufa ku chiwerewere,* zinthu zodetsa, chilakolako chosalamulirika cha kugonana,+ kulakalaka zinthu zoipa komanso dyera limene ndi kulambira mafano.
13 Chifukwa ngati mukukhala motsatira zofuna za thupi, ndiye kuti mosakayikira mudzafa.+ Koma mukalola kuti mphamvu ya mzimu ikuthandizeni kupha zochita za thupi, mudzakhala ndi moyo.+
5 Choncho chititsani ziwalo za thupi lanu+ padziko lapansi kukhala zakufa ku chiwerewere,* zinthu zodetsa, chilakolako chosalamulirika cha kugonana,+ kulakalaka zinthu zoipa komanso dyera limene ndi kulambira mafano.