Machitidwe 17:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno anthuwo atamva za kuuka kwa akufa, ena anayamba kuseka mwachipongwe,+ pomwe ena anati: “Chabwino, udzatiuzenso zimenezi nthawi ina.”
32 Ndiyeno anthuwo atamva za kuuka kwa akufa, ena anayamba kuseka mwachipongwe,+ pomwe ena anati: “Chabwino, udzatiuzenso zimenezi nthawi ina.”