Numeri 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako gulu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo Aisiraeli nawonso anayamba kulira nʼkumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+ Numeri 11:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Malo amenewo anawatchula kuti Kibiroti-hatava,*+ chifukwa anakwirirapo anthu amene anasonyeza mtima wadyera.+
4 Kenako gulu la anthu a mitundu yosiyanasiyana+ lomwe linali pakati pawo linasonyeza mtima wadyera,+ ndipo Aisiraeli nawonso anayamba kulira nʼkumanena kuti: “Ndani atipatse nyama yoti tidye?+
34 Malo amenewo anawatchula kuti Kibiroti-hatava,*+ chifukwa anakwirirapo anthu amene anasonyeza mtima wadyera.+