6 Amene amaona kuti tsiku lina ndi lofunika amachita zimenezo pofuna kulemekeza Yehova. Amene amadya chakudya chilichonse, amadya kuti alemekeze Yehova,+ chifukwa amayamika Mulungu. Amene sadya, nayenso sadya pofuna kulemekeza Yehova, chifukwa amayamikanso Mulungu.+