Aroma 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Nʼchifukwa chake Khristu anafa nʼkukhalanso ndi moyo, kuti akhale Ambuye wa akufa ndiponso wa amoyo.+ Aefeso 4:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma tizilankhula zoona ndiponso kusonyeza chikondi. Tikatero tidzakhala achikulire mʼzinthu zonse ndipo tidzatha kuchita zinthu mogwirizana ndi Khristu, amene ndi mutu.+ Akolose 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Simukusowa kalikonse chifukwa cha iye, amene ndi mutu wa boma lililonse ndi ulamuliro uliwonse.+
9 Nʼchifukwa chake Khristu anafa nʼkukhalanso ndi moyo, kuti akhale Ambuye wa akufa ndiponso wa amoyo.+
15 Koma tizilankhula zoona ndiponso kusonyeza chikondi. Tikatero tidzakhala achikulire mʼzinthu zonse ndipo tidzatha kuchita zinthu mogwirizana ndi Khristu, amene ndi mutu.+