26 Ndiyeno zizikhala bwanji abale? Mukasonkhana pamodzi, wina akhoza kukhala ndi salimo, wina chiphunzitso, wina mawu amene walandira kuchokera kwa Mulungu komanso wina akhoza kulankhula malilime wina nʼkumamasulira.+ Muzichita zonsezi kuti mulimbikitsane.