Yohane 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Patapita masiku 8, ophunzira akewo analinso mʼnyumba ndipo Tomasi anali nawo limodzi. Yesu analowa ngakhale kuti zitseko zinali zokhoma ndipo anaimirira pakati pawo nʼkunena kuti: “Mtendere ukhale nanu.”+
26 Patapita masiku 8, ophunzira akewo analinso mʼnyumba ndipo Tomasi anali nawo limodzi. Yesu analowa ngakhale kuti zitseko zinali zokhoma ndipo anaimirira pakati pawo nʼkunena kuti: “Mtendere ukhale nanu.”+