Machitidwe 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma iye anawauza ndi manja kuti akhale chete, ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Yehova* anamutulutsira mʼndende. Kenako anati: “Nkhani imeneyi mukauze Yakobo+ ndi abale.” Atatero anatuluka nʼkupita kwina.
17 Koma iye anawauza ndi manja kuti akhale chete, ndipo anawafotokozera mwatsatanetsatane mmene Yehova* anamutulutsira mʼndende. Kenako anati: “Nkhani imeneyi mukauze Yakobo+ ndi abale.” Atatero anatuluka nʼkupita kwina.