-
Machitidwe 7:59Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
59 Pamene ankamuponya miyala, Sitefano anapempha mochonderera kuti: “Ambuye Yesu, landirani mzimu wanga.”
-
-
1 Akorinto 15:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Komanso ngati Khristu sanaukitsidwe, kulalikira kwathu nʼkopanda phindu, ndipo chikhulupiriro chanu nʼchopandanso phindu.
-