17 Imfa inalamulira ngati mfumu chifukwa cha uchimo wa munthu mmodziyo.+ Koma anthu amene alandira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu ndiponso mphatso yake yaulere ya chilungamo,+ adzakhala ndi moyo kuti alamulire ngati mafumu+ kudzera mwa munthu mmodziyu, Yesu Khristu.+