Mateyu 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atakhala pansi mʼphiri la Maolivi, ophunzira anabwera kwa iye ali payekha nʼkumufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino+ chidzakhala chiyani?” 1 Atesalonika 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa Ambuyewo adzatsika kuchoka kumwamba ndi mfuu yolamula. Mawu awo adzamveka kuti ndi a mkulu wa angelo+ ndipo adzanyamula lipenga la Mulungu mʼdzanja lawo. Ndipo amene anafa mwa Khristu adzakhala oyambirira kuuka.+
3 Atakhala pansi mʼphiri la Maolivi, ophunzira anabwera kwa iye ali payekha nʼkumufunsa kuti: “Tiuzeni, kodi zinthu zimenezi zidzachitika liti, ndipo chizindikiro cha kukhalapo* kwanu+ ndi cha mapeto a nthawi* ino+ chidzakhala chiyani?”
16 Chifukwa Ambuyewo adzatsika kuchoka kumwamba ndi mfuu yolamula. Mawu awo adzamveka kuti ndi a mkulu wa angelo+ ndipo adzanyamula lipenga la Mulungu mʼdzanja lawo. Ndipo amene anafa mwa Khristu adzakhala oyambirira kuuka.+