Yohane 14:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mwamva ndikukuuzani kuti, ‘Ndikupita ndipo ndidzabweranso kwa inu.’ Ngati mumandikonda, mukanasangalala kuti ndikupita kwa Atate wanga, chifukwa Atate ndi wamkulu kuposa ine.+
28 Mwamva ndikukuuzani kuti, ‘Ndikupita ndipo ndidzabweranso kwa inu.’ Ngati mumandikonda, mukanasangalala kuti ndikupita kwa Atate wanga, chifukwa Atate ndi wamkulu kuposa ine.+