Miyambo 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+Koma amene amachita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+ 1 Akorinto 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kudzitama kwanu si kwabwino. Kodi simukudziwa kuti zofufumitsa zapangʼono zimafufumitsa mtanda wonse wa ufa wokandakanda?+
20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+Koma amene amachita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+
6 Kudzitama kwanu si kwabwino. Kodi simukudziwa kuti zofufumitsa zapangʼono zimafufumitsa mtanda wonse wa ufa wokandakanda?+