Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+ 1 Akorinto 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho musaweruze+ chilichonse nthawi isanakwane, mpaka Ambuye adzafike. Iye adzachititsa kuti zinsinsi zamumdima zionekere komanso adzaonetsa poyera zimene zili mumtima. Ndiyeno aliyense payekha adzayamikiridwa ndi Mulungu.+ Chivumbulutso 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Taonani! Ndikubwera mofulumira ndipo ndili ndi mphoto yoti ndipereke kwa aliyense mogwirizana ndi ntchito yake.+
5 Choncho musaweruze+ chilichonse nthawi isanakwane, mpaka Ambuye adzafike. Iye adzachititsa kuti zinsinsi zamumdima zionekere komanso adzaonetsa poyera zimene zili mumtima. Ndiyeno aliyense payekha adzayamikiridwa ndi Mulungu.+
12 ‘Taonani! Ndikubwera mofulumira ndipo ndili ndi mphoto yoti ndipereke kwa aliyense mogwirizana ndi ntchito yake.+