Ezekieli 20:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Chifukwa cha kafungo kosangalatsa,* ndidzasangalala nanu ndikadzakutulutsani pakati pa anthu a mitundu ina nʼkukusonkhanitsani pamodzi kuchokera mʼmayiko osiyanasiyana kumene munabalalikira.+ Komanso ndidzakusonyezani kuti ndine woyera ndipo anthu a mitundu ina adzaona zimenezi.+ 2 Akorinto 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Okondedwa, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi ndi mzimu,+ kuti tikhale oyera pamene tikuopa Mulungu.
41 Chifukwa cha kafungo kosangalatsa,* ndidzasangalala nanu ndikadzakutulutsani pakati pa anthu a mitundu ina nʼkukusonkhanitsani pamodzi kuchokera mʼmayiko osiyanasiyana kumene munabalalikira.+ Komanso ndidzakusonyezani kuti ndine woyera ndipo anthu a mitundu ina adzaona zimenezi.+
7 Okondedwa, popeza talonjezedwa zinthu zimenezi,+ tiyeni tidziyeretse ndipo tichotse chinthu chilichonse choipitsa thupi ndi mzimu,+ kuti tikhale oyera pamene tikuopa Mulungu.