-
2 Akorinto 9:1, 2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ponena za utumiki wothandiza oyerawo,+ nʼzosafunika kuti ndichite kukulemberani. 2 Chifukwa ndikudziwa kuti muli ndi mtima wofunitsitsa ndipo ndikunena zimenezi monyadira kwa anthu a ku Makedoniya. Ndikumawauza kuti abale a ku Akaya akhala okonzeka kwa chaka chimodzi tsopano, ndipo kudzipereka kwanu kwalimbikitsa abale ambiri kumeneko.
-