Machitidwe 13:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma Ayuda anauza zoipa amayi otchuka oopa Mulungu komanso amuna olemekezeka amumzindawo. Choncho iwo anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo.
50 Koma Ayuda anauza zoipa amayi otchuka oopa Mulungu komanso amuna olemekezeka amumzindawo. Choncho iwo anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo.