15 Koma ine ndinati: ‘Ambuye, ndinu ndani kodi?’ Ndipo Ambuye anati: ‘Ndine Yesu amene iwe ukumuzunza. 16 Komabe dzuka ndipo uimirire. Ndaonekera kwa iwe kuti ndikusankhe kuti ukhale mtumiki komanso mboni ya zinthu zonse zokhudza ine, zomwe waona ndiponso zimene ndidzakuonetsa.+