Aroma 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mdulidwe+ ndi waphindu pokhapokha ngati iweyo umatsatiradi Chilamulo.+ Koma ngati umaphwanya Chilamulo, mdulidwe wako ndi wopanda ntchito. Agalatiya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Onse amene amadalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Munthu aliyense amene sakupitiriza kutsatira zinthu zonse zimene zinalembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi wotembereredwa.”+
25 Mdulidwe+ ndi waphindu pokhapokha ngati iweyo umatsatiradi Chilamulo.+ Koma ngati umaphwanya Chilamulo, mdulidwe wako ndi wopanda ntchito.
10 Onse amene amadalira ntchito za chilamulo ndi otembereredwa, chifukwa Malemba amati: “Munthu aliyense amene sakupitiriza kutsatira zinthu zonse zimene zinalembedwa mumpukutu wa Chilamulo ndi wotembereredwa.”+