Miyambo 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuyankha modekha* kumabweza mkwiyo,+Koma mawu opweteka amayambitsa mkwiyo.+ Akolose 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho monga anthu osankhidwa ndi Mulungu,+ oyera ndi okondedwa, valani chifundo chachikulu,+ kukoma mtima, kudzichepetsa,+ kufatsa+ komanso kuleza mtima.+ 1 Timoteyo 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma munthu wa Mulungu iwe, thawa zinthu zimenezi. Mʼmalomwake yesetsa kukhala wachilungamo, wodzipereka kwa Mulungu, wachikhulupiriro, wachikondi, wopirira ndiponso wofatsa.+ Tito 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Asamanenere zoipa munthu aliyense ndiponso asamakonde kukangana. Koma akhale ololera+ ndipo azikhala ofatsa kwa anthu onse.+
12 Choncho monga anthu osankhidwa ndi Mulungu,+ oyera ndi okondedwa, valani chifundo chachikulu,+ kukoma mtima, kudzichepetsa,+ kufatsa+ komanso kuleza mtima.+
11 Koma munthu wa Mulungu iwe, thawa zinthu zimenezi. Mʼmalomwake yesetsa kukhala wachilungamo, wodzipereka kwa Mulungu, wachikhulupiriro, wachikondi, wopirira ndiponso wofatsa.+
2 Asamanenere zoipa munthu aliyense ndiponso asamakonde kukangana. Koma akhale ololera+ ndipo azikhala ofatsa kwa anthu onse.+