Levitiko 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usamadane ndi mʼbale wako mumtima mwako,+ koma uzimudzudzula+ kuti iwenso usakhale wochimwa ngati iyeyo. Akolose 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pitirizani kulolerana ndi kukhululukirana ndi mtima wonse,+ ngakhale pamene wina ali ndi chifukwa chodandaulira za mnzake.+ Mofanana ndi Yehova* amene anakukhululukirani ndi mtima wonse, inunso muzichita chimodzimodzi.+
17 Usamadane ndi mʼbale wako mumtima mwako,+ koma uzimudzudzula+ kuti iwenso usakhale wochimwa ngati iyeyo.
13 Pitirizani kulolerana ndi kukhululukirana ndi mtima wonse,+ ngakhale pamene wina ali ndi chifukwa chodandaulira za mnzake.+ Mofanana ndi Yehova* amene anakukhululukirani ndi mtima wonse, inunso muzichita chimodzimodzi.+