13 Koma inunso munakhala ndi chiyembekezo mwa iye mutamva mawu a choonadi, omwe ndi uthenga wabwino wonena za chipulumutso chanu. Mutakhulupirira, Mulungu anagwiritsa ntchito mzimu woyera umene analonjeza kuti akuikeni chidindo+ ndipo anagwiritsa ntchito Khristu kuti achite zimenezi.