2 Timoteyo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Tukiko+ ndamutuma ku Efeso. Tito 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikadzatuma Atema kapena Tukiko+ kwa iwe, udzayesetse kuti udzandipeze ku Nikopoli, chifukwa ndaganiza zokakhala kumeneko nyengo yozizirayi.
12 Ndikadzatuma Atema kapena Tukiko+ kwa iwe, udzayesetse kuti udzandipeze ku Nikopoli, chifukwa ndaganiza zokakhala kumeneko nyengo yozizirayi.